Romans 9:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Mulungu adauza Rebeka kuti, “Wamkuluyu adzatumikira wamng'onoyu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chotero kunanenedwa kwa uyo, Wamkulu adzakhala kapolo wa wamng'ono.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
osati chifukwa cha ntchito za munthu koma chifuniro cha Iye mwini, anawuza Rebeka kuti, “Wamkulu adzatumikira wamʼngʼono.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cotero kunanenedwa kwa uyo, Wamkuru adzakhala kapolo wa wamng'ono.