Romans 9:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono kapena wina nkundifunsa kuti, “Ngati zili choncho, chifukwa chiyani Mulungu akuŵadzudzulabe anthu? Nanga ndani angaletse Mulungu kuchita zimene Iye afuna?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo udzanena ndine kodi, Adandaulabe bwanji? Pakuti ndani anakaniza chifuno chake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono mmodzi wa inu nʼkundifunsa kuti, “Nanga nʼchifukwa chiyani Mulungu amatipeza olakwa? Nanga ndani amene amakana chifuniro chake?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo udzanena ndine kodi, Adandaulabe bwanji? Pakuti ndani anakaniza cifuno cace?