Romans 9:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndili ndi chisoni chachikulu. Ndipo ukundipweteka kosalekeza chifukwa cha abale anga, anthu a mtundu wangaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti ndagwidwa ndi chisoni chachikulu ndi kuphwetekwa mtima kosaleka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndili ndi chisoni chachikulu ndipo ndikumva kupwetekeka kosalekeza mu mtima mwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti ndagwidwa ndi cisoni cacikuru ndi kuphwetekwa mtima kosaleka.