Romans 9:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu adaafunanso kuti udziŵike ulemerero wake waukulu pa ife, amene Iye adatichitira chifundo, natikonzeratu kuti tilandire ulemerero.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi kuti Iye akadziwitse ulemerero wake waukulu pa zotengera zachifundo, zimene Iye anazikonzeratu kuulemerero,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anachita izi kufuna kuonetsa kulemera kwa ulemerero wake ndi kuti udziwike kwa amene analandira chifundo chake. Iye anawakonzeratu kuti alandire ulemerero wake
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kuti iye akadziwitse ulemerero wace waukuru pa zotengera zacifundo, zimene iye anazikonzeratu kuulemerero,