Romans 9:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pajatu ife ndife amene Mulungu adatiitana, osati kuchokera kwa Ayuda okha ai, komanso kuchokera kwa anthu a mitundu ina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi ife amenenso Iye anatiitana, si a mwa Ayuda okhaokha, komanso a mwa anthu amitundu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngakhale ifenso amene anatiyitana osati kuchokera kwa Ayuda okha komanso kwa a mitundu ina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi ife amenenso iye anatiitana, si a mwa Ayuda okha okha, komanso a mwa anthu amitundu?