Romans 9:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo kumalo komwe iwo adauzidwa kuti, ‘Sindinu mtundu wanga’, kumeneko adzatchedwa ‘Ana a Mulungu wopatsa moyo.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudzali, kuti pamalo pamenepo kunanenedwa kwa iwo, Simuli anthu anga ai, pomwepo iwo adzatchedwa ana a Mulungu wamoyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo, “Pamalo omwewo pamene ananena kuti, ‘Sindinu anthu anga,’ pomweponso adzawatchula kuti, ‘Ana a Mulungu wamoyo.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
1 Ndipo kudzali, kuti pamalo pamenepo kunanenedwa kwa iwo, Simuli anthu anga ai, Pomwepo iwo adzachedwa ana a Mulungu wamoyo.