Romans 9:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti Ambuye adzagamula milandu ya anthu pa dziko lapansi. Ndipo adzachita zimenezi mofulumira ndi mwachidule.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Ambuye adzachita mau ake pa dziko lapansi, kuwatsiriza mwachidule.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Ambuye adzagamula milandu ya anthu pa dziko lapansi mofulumira ndi kumaliziratu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Ambuye adzacita mau ace pa dziko lapansi, kuwatsiriza mwacidule.