Romans 9:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Izi zili monga momwe Yesaya adaaneneratunso kale kuti, “Ambuye amphamvuzonse akadapanda kutisiyirako zidzukulu zina, tikadafafanizidwa ngati Sodomu ndi Gomora.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo monga Yesaya anati kale, Ngati Ambuye wa makamu a kumwamba sanatisiyira ife mbeu, tikadakhala monga Sodomu, ndipo tikadafanana ndi Gomora.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga momwe Yesaya ananena malo ena kuti, “Ngati Yehova Wamphamvuzonse akanapanda kutisiyira zidzukulu, ife tikanawonongeka ngati anthu a ku Sodomu, tikanakhala ngati anthu a ku Gomora.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo monga Yesaya anati kale, 4 Ngati Ambuye wa makamu a kumwamba sanatisiyira ife mbeu, Tikadakhala monga Sodoma, ndipo tikadafanana ndi Gomora.