Romans 9:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
monga Malembo anenera kuti, “Inetu ndikuika m'Ziyoni mwala wodzakhumudwitsa anthu, thanthwe limene lidzaŵagwetsa. Koma wokhulupirira Iyeyo, sadzachita manyazi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
monganso kwalembedwa, kuti, Onani, ndikhazika m'Ziyoni mwala wakukhumudwa nao, ndi thanthwe lophunthwitsa; ndipo wakukhulupirira Iye sadzachita manyazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga momwe kwalembedwa kuti, “Taonani, Ine ndikuyika mwala mu Ziyoni wopunthwitsa anthu, thanthwe limene limagwetsa anthu. Koma amene akhulupirira Iye sadzachititsidwa manyazi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
monganso kwalembedwa, kuti, 8 Onani, ndikhazika m'Ziyoni mwala wakukhumudwa nao, ndi thanthwe lopunthwitsa; Ndipo 9 wakukhulupirira iye sadzacita manyazi.