Romans 9:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sindiye kutitu Mulungu sadasunge malonjezo ai. Pakuti si anthu onse obadwa mu mtundu wa Aisraele amene ali Aisraele enieni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma sikuli ngati mau a Mulungu anakhala chabe ai. Pakuti onse akuchokera kwa Israele siali Israele;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sikuti mawu a Mulungu analephera. Pakuti si onse obadwa mwa Israeli amene ndi Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma sikuli ngati mau a Mulungu anakhala cabe ai. Pakuti onse akucokera kwa a Israyeli siali Israyeli;