Romans 9:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye kuti si zidzukulu zonse za Abrahamu zimene zili ana a Mulungu. Koma Mulungu adauza Abrahamu kuti, “Ana a Isaki okha ndiwo adzatchedwa zidzukulu zako.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kapena chifukwa ali mbeu ya Abrahamu, siali onse ana; koma anati, Mwa Isaki, mbeu yako idzaitanidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kapena kuti ana ake chifukwa anachokera mwa Abrahamu. Koma zidzukulu zako zidzachokera mwa Isake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kapena cifukwa ali mbeu ya Abrahamu, siali onse ana; koma anati, Mwa Isake, mbeu yako idzaitanidwa.