Romans 9:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye kuti, si ana onse a Abrahamu amene ali ana a Mulungu ai. Zidzukulu zake zenizeni ndi ana okhawo amene adabadwa potsata lonjezo la Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiko kuti, ana a thupi sakhala iwo ana a Mulungu ai; koma ana a lonjezo awerengedwa mbeu yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kutanthauza kuti, si ana obadwa mʼthupi amene ndi ana a Mulungu koma ndi ana a lonjezano amene amatengedwa kukhala zidzukulu za Abrahamu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiko kuti, ana a thupi sakhala iwo ana a Mulungu ai; koma ana a lonjezo awerengedwa mbeu yace.