Ruth 1:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
nauza Naomiyo kuti, “Iyai, ife tipita nao kwa anthu akwanu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ananena naye, Iai, koma tidzapita nanu kwa anthu a kwanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anati kwa Naomi, “Ife tipita nawo kwa anthu akwanu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ananena naye, Iai, koma tidzapita nanu kwa anthu a kwanu.