Ruth 1:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Naomi adaŵauza kuti, “Pepani ana anga, bwererani kwanu. Chifukwa chiyani mukufuna kupita nao? Kodi mukuganiza kuti ndingathe kubala ana ena aamuna, kuti adzakhale amuna anu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati Naomi, Bwererani, ana anga, mudzatsagana nane bwanji? Ngati ndili nao m'mimba mwanga ana amuna ena kuti akhale amuna anu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Naomi anati, “Bwererani kwanu ana anga. Chifukwa chiyani mukufuna kupita ndi ine? Kodi ine ndingaberekenso ana ena kuti akhale amuna anu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati Naomi, Bwererani, ana anga, mudzatsagana nane bwanji? ngati ndiri nao m'mimba mwanga ana amuna ena kuti akhale amuna anu?