Ruth 1:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kodi tsono mukadatha kudikira mpaka akule? Kodi zimenezi zikadakuletsani kukwatiwa? Ai, ana anga, zotere zikadandiŵaŵa kwambiri chifukwa cha inu, poona kuti sindinu koma ndine amene Chauta adafuna kuti ndizunzike.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kodi mudzawalindirira akakula? Mudzadziletsa osakwatibwa? Iai, ana anga, pakuti chandiwawa koposa chifukwa cha inu popeza dzanja la Yehova landitulukira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kodi inu mukanadikira kuti akule? Kodi mukanakhalabe osakwatiwa kudikira iwowo? Ayi ana anga. Zimenezi zikundiwawa kwambiri kuposa inu, chifukwa ndi ineyo amene Yehova wafuna kuti ndizunzike.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kodi mudzawalindirira akakula? mudzadziletsa osakwatibwa? Iai, ana anga, pakuti candiwawa koposa cifukwa ca inu popeza dzanja la Yehova landiturukira.