Ruth 1:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo iwo aja adayambanso kulira mokweza. Olipa adampsompsona mpongozi wake ndi kumulaŵira, koma Rute adakangamira Naomiyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nakweza iwo mau ao, naliranso misozi; ndi Oripa anampsompsona mpongozi wake, koma Rute anamkangamira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atamva zimenezi analiranso kwambiri, ndipo Oripa anapsompsona apongozi ake nawatsanzika, koma Rute anakakamirabe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nakweza iwo mau ao, naliranso misozi; ndi Olipa anampsompsona mpongozi wace, koma Rute anamkangamira.