Ruth 1:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumene inu mukafere, inenso ndikafera komweko ndi kuikidwa komweko. Chauta andichite choipa chilichonse chingakule motani, ngati kanthu kena kalikonse katisiyanitse, kupatula imfa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kumene mudzafera inu ine ndidzafera komweko, ndi kuikidwa komweko; andilange Yehova naonjezeko, chilichonse chikasiyanitsa inu ndi ine, koma imfa ndiyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumene mukafere inenso ndidzafera komweko ndipo komweko ndikayikidwa mʼmanda. Yehova andichite choyipa chingakule motani, ngati china chingatirekanitse ife kupatula imfa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kumene mudzafera inu ine ndidzafera komweko, ndi kuikidwa komweko; andilange Yehova naonjezeko, ciri conse cikasiyanitsa inu ndi ine, koma imfa ndiyo.