Ruth 1:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Naomi ataona kuti Rute watsimikiza kupita nao, sadanenenso kanthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pakuona kuti analimbika kumuka naye, analeka kulankhula naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Naomi atazindikira kuti Rute watsimikiza kupita naye, analeka kumukakamiza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pakuona kuti analimbika kumuka naye, analeka kulankhula naye.