Ruth 1:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Elimeleki mwamuna wa Naomi adamwalira, ndipo Naomiyo adatsala ndi ana aŵiri aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Elimeleki mwamuna wake wa Naomi anamwalira; natsala iye ndi ana ake awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Elimeleki, mwamuna wake wa Naomi anamwalira ndipo Naomiyo anatsala ndi ana ake aamuna awiri aja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Elimeleki mwamuna wace wa Naomi anamwalira; natsala iye ndi ana ace awiri.