Ruth 1:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Maloni ndi Kiliyoni adamwalira, kotero kuti Naomi adataya ana ake aŵiri aja, pamodzi ndi mwamuna wake yemwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Maloni ndi Kilioni anamwalira onse awiri; motero ana ake amuna awiri ndi mwamuna wake anamsiya mkaziyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Maloni ndi Kiliyoni anamwaliranso kotero kuti Naomi anatsala yekha wopanda ana ake awiri aja ndi mwamuna wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Maloni ndi Kilioni anamwalira onse awiri; motero ana ace amuna awiri ndi mwamuna wace anamsiya mkaziyo.