Ruth 2:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Naomi anali ndi wachibale wake wachuma kwambiri, wa m'banja la malemu mwamuna wake uja Elimeleki, dzina lake Bowazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Naomi anali naye mbale wa mwamuna wake, ndiye munthu mwini chuma chambiri wa banja la Elimeleki; dzina lake ndiye Bowazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Naomi anali ndi mʼbale wake wolemera kwambiri wochokera ku banja la mwamuna wake Elimeleki, dzina lake Bowazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Naomi anali nave mbale wa mwamuna wace, ndiye munthu mwini cuma cambiri wa banja la Elimeleki; dzina lace ndiye Boazi.