Ruth 2:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Rute adaŵerama, nazyolikitsa nkhope pansi, ndipo adafunsa kuti, “Chifukwa chiyani ndapeza kukoma mtima kotereku mwa inu, kuti mulabadeko za ine mlendo?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero anagwa nkhope yake pansi, nadziweramira pansi, nanena naye, Mwandikomera mtima chifukwa ninji kuti mundisamalira ine, popeza ndine mlendo?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atamva zimenezi Rute anawerama nazolikitsa nkhope yake pansi. Kenaka anafunsa kuti, “Mwandikomera mtima chotere mlendo ngati ine chifukwa chiyani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero anagwa nkhope yace pansi, nadziweramira pansi, nanena naye, Mwandikomera mtima cifukwa ninji kuti mundisamalira ine, popeza ndine mlendo?