Ruth 2:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muzimusololerako ngala zina zam'mitolo ndi kumlekera kuti azikunkha, osamdzudzula.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiponso mumtayire za m'manja, ndi kuzisiya, natole khunkha, osamdzudzula.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma muzimusololerako ngala zina za mʼmitolo ndi kumusiyira kuti azikunkha ndipo musamukalipire.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiponso mumtayire za m'manja, ndi kuzisiya, natole khunkha, osamdzudzula.

Recommended Reading