Ruth 2:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Naomi adauza Rute kuti, “Kuli bwino mwana wanga kuti uzipita ndi adzakazi ake, kuwopa kuti ukapita m'munda wina, angakuvute.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati Naomi kwa Rute mpongozi wake, Nchabwino, mwana wanga, kuti uzituluka nao adzakazi ake, ndi kuti asakukomane m'munda wina uliwonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Naomi anati kwa Rute mpongozi wake, “Kuli bwino mwana wanga kuti uzipita ndi adzakazi ake kuopa kuti mʼmunda wa munthu wina angakuvute.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati Naomi kwa Rute mpongozi wace, Ncabwino, mwana wanga, kuti uzituruka nao adzakazi ace, ndi kuti asakukomane m'munda wina uti wonse.