Ruth 2:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Bowazi adafunsa kapitao wake amene ankayang'anira anthu okolola aja kuti, “Kodi mai uyu ndani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati Bowazi kwa mnyamata woyang'anira ochekawo, Mkazi uyu ngwa yani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Bowazi anafunsa kapitawo wake amene ankayangʼanira okolola aja kuti, “Mayi uyo ndi ndani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati Boazi kwa mnyamata wace woyang'anira ocekawo, Mkazi uyu ngwa yani?