Ruth 2:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kapitao wakeyo adayankha kuti, “Maiyu ndi Mmowabu amene adabwera ndi Naomi kuchokera ku dziko la Mowabu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mnyamata woyang'anira ochekawo anayankha nati, Ndiye mkazi Mmowabuyo anabwera ndi Naomi ku dziko la Mowabu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kapitawo uja anayankha kuti, “Mayiyu ndi Mmowabu amene anabwera ndi Naomi kuchokera ku dziko la Mowabu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mnyamata woyang'anira ocekawo anayankha nati, Ndiye mkazi Mmoabuyo anabwera ndi Naomi ku dziko la Moabu;