Ruth 3:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku lina Naomi adafunsa Rute kuti, “Kodi iwe mwana wanga, nanga sikwabwino kuti ndikupezere pokhala, kuti zinthu zizikuyendera bwino?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Naomi mpongozi wake ananena naye, Mwana wanga, kodi ndisakufunire popumulako, kuti ukhale bwino?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku lina Naomi anafunsa mpongozi wake Rute kuti, “Mwana wanga, kodi si kwabwino kuti ndikupezere kokhala kuti zinthu zizikuyendera bwino?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Naomi mpongozi wace ananena naye, Mwana wanga, kodi ndisakufunire popumulako, kuti ukhale bwino?