Ruth 3:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsopano usadandaule, mwana wanga. Ndidzakuchitira zonse zimene upemphe, pakuti anzanga am'mudzimu akudziŵa kuti ndiwe mkazi wabwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo tsopano, mwana wanga, usaope; ndidzakuchitira zonse unenazi; pakuti onse a pa mudzi wa anthu a mtundu wanga adziwa kuti iwe ndiwe mkazi waulemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo tsopano mwana wanga usaope. Ine ndidzakuchitira chilichonse udzapemphe popeza anzanga onse amʼmudzi muno akudziwa kuti ndiwe mkazi wa khalidwe labwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo tsopano, mwana wanga, usaope; ndidzakucitira zonse unenazi; pakuti onse a pa mudzi wa anthu a mtundu wanga adziwa kuti iwe ndiwe mkazi waulemu.