Ruth 3:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atafika kwa mpongozi wake uja, mpongoziyo adati, “Zinthu zakuyendera bwanji, mwana wanga?” Rute adamfotokozera zonse zimene munthu uja adamchitira,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene anadza kwa mpongozi wake, iye anati, Wapeza bwanji, mwana wanga? Pamenepo anamfotokozera zonse anamchitira munthuyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Rute atafika kwa apongozi ake anamufunsa kuti, “Zinayenda bwanji mwana wanga?” Kenaka iye anafotokoza zonse zimene Bowazi anamuchitira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene anadza kwa mpongozi wace, iye anati, Wapeza bwanji, mwana wanga? Pamenepo anamfotokozera zonse anamcitira munthuyo.