Ruth 3:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo adati, “Wandipatsa makilogramu makumi aŵiri a barele, nandiwuza kuti, ‘Usapite kwa apongozi ako chimanjamanja.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Natinso, Miyeso, iyi isanu ndi umodzi ya barele anandipatsa, pakuti anati, Usafike kwa mpongozi wako wopanda kanthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anati, “Munthuyo anandipatsa makilogalamu makumi awiri awa a barele, nandiwuza kuti usapite kwa apongozi ako wopanda kanthu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Natinso, Miyeso iyi isanu ndi umodzi ya barele anandipatsa, pakuti anati, Usafike kwa mpongozi wako wopanda kanthu.