Ruth 3:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bowazi amene adzakazi ake unali nawo, ndi wachibale wathu. Usiku uno iye akhala akupuntha barele ku malo ake opunthira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nanga Bowazi wodziwana nafe, amene unakhala nao adzakazi ake? Taona, usiku uno apuntha barele popunthirapo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Bowazi amene adzakazi ake wakhala nawo nthawi yonseyi, si wachibale wathu kodi? Usiku uno akhala akupeta barele ku malo opunthira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nanga Boazi wodziwana nafe, amene unakhala nao adzakazi ace? Taona, usiku uno apuntha barele popunthirapo.