Ruth 3:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Rute adayankha kuti, “Zonse mwanenazi ndichita.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ananena naye, Zonse muzinena ndidzachita.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Rute anayankha kuti, “Ndichita zonse zimene mwanena.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ananena naye, Zonse muzinena ndidzacita.