Ruth 3:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono pakati pa usiku Bowazi adadzidzimuka natembenuka, naona mkazi atagona ku mapazi ake. Adafunsa kuti, “Ndiwe yani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, pakati pa usiku munthuyo anadzidzimuka, natembenuka; ndipo taona pa mapazi ake pagona mkazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono pakati pa usiku Bowazi anadzidzimuka, natembenuka, ndipo anangoona mkazi akugona ku mapazi ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, pakati pa usiku munthuyo anadzidzimuka, natembenuka; ndipo taona pa mapazi ace pagona mkazi.