Ruth 4:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndatenganso Rute Mmowabu uja, mkazi wa malemu Maloni, kuti akhale mkazi wanga, kuti dzina la malemulo lisungike pa choloŵa chake, ndipo lisafafanizike pakati pa abale ake ndiponso m'mudzi mwake. Nonsenu ndinu mboni lero lino.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiponso Rute Mmowabu, mkazi wa Maloni ndamgula akhale mkazi wanga kuukitsa dzina la wakufayo pa cholowa chake; kuti dzina la wakufayo lisaiwalike pakati pa abale ake, ndi pa chipata cha malo ake; inu ndinu mboni lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndatenganso Rute Mmowabu uja mkazi wa malemu Maloni, kuti akhale mkazi wanga, kuti dzina la malemu Maloni lisungike pa cholowa chake, ndipo lisafafanizike pakati pa abale ake ngakhalenso mʼmudzi mwake. Nonsenu ndinu mboni lero lino.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiponso Rute Mmoabu, mkazi wa Maloni ndamgula akhale mkazi wanga kuukitsa dzina la wakufayo pa colowa cace; kuti dzina la wakufayo lisaiwalike pakati pa abale ace, ndi pa cipata ca malo ace; inu ndinu mboni lero lino.