Ruth 4:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana ako amene Chauta adzakupatse mwa mai ameneyu, adzamange banja longa la Perezi, amene Tamara adabalira Yuda.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi nyumba yako inge nyumba ya Perezi, amene Tamara anambalira Yuda, ndi mbeu imene Yehova adzakupatsa ya namwali uyu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana amene Yehova adzakupatsa mwa mkaziyu adzamange banja lako kukhala la Perezi, amene Tamara anamubalira Yuda.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi nyumba yako inge nyumba ya Perezi, amene Tamare anambalira Yuda, ndi mbeu imene Yehova adzakupatsa ya namwali uyu.