Ruth 4:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Naomi adanyamula mwanayo namfukata ndipo adakhala mlezi wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Naomi anamtenga mwanayo, namuika pachifuwa pake, nakhala mlezi wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Naomi anatenga mwanayo namufukata ndipo anakhala mlezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Naomi anamtenga mwanayo, namuika pacifuwa pace, nakhala mlezi wace.