Ruth 4:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akazi achinansi ake adalengeza kuti, “Mwana wabadwa kwa Naomi.” Ndipo adamutcha dzina loti Obedi. Iyeyu adakhala bambo wake wa Yese, bambo wa Davide.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi akazi anansi ake anamutcha dzina, ndi kuti, Kwa Naomi kwambadwira mwana; namutcha dzina lake Obedi; ndiye atate wa Yese atate wa Davide.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amayi achinansi ake anati, “Naomi ali ndi mwana wamwamuna.” Ndipo anamutcha dzina lake Obedi. Iye anali abambo a Yese abambo ake a Davide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi akazi anansi ace anamucha dzina, ndi kuti, Kwa Naomi kwambadwira mwana; namucha dzina lace Ohedi; ndiye atate wa Jese atate wa Davide.