Song of Solomon 1:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Masaya ako akukongola ndi ndolo zam'makutuzi. Khosi lakonso likukongola ndi mikanda ya miyala yamtengowapatali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masaya ako akongola ndi nkhata zatsitsi, ndi khosi lako ndi zinganga za mkanda wonyezimira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Masaya ako ndi okongola ndi ndolo zamʼmakutuzo, khosi lako likukongola ndi mikanda yamiyala yamtengowapatali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masaya ako akongola ndi nkhata zatsitsi, Ndi khosi lako ndi zinganga za mkanda wonyezimira.