Song of Solomon 1:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wokondedwa wanga ndikumuwona ngati kathumba ka mure, kamene kamakhala pakati pa maŵere angaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wokondedwa wanga mnyamatayo ali kwa ine ngati thumba la mure, logona pakati pa mawere anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wokondedwa wanga ali ngati kathumba ka mure kwa ine, kamene kamakhala pakati pa mawere angawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wokondedwa wanga mnyamatayo ali kwa ine ngati thumba la nipa, Logona pakati pa maere anga.