Song of Solomon 1:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wokondedwa wanga ndikumuwona ngati chipukutu cha maluŵa ofiira a m'munda wamphesa wa ku Engedi. Mwamuna
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wokondedwa wanga ali kwa ine ngati chipukutu cha maluwa ofiira m'minda yamipesa ya ku Engedi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wokondedwa wanga ali ngati mpukutu wa maluwa ofiira, ochokera ku minda ya mpesa ya ku Eni-Gedi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wokondedwa wanga ali kwa ine ngati cipukutu ca maluwa ofiira M'minda yamipesa ya ku Engedi.