Song of Solomon 1:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe bwenzi langa, ndiwe wokongola, ndiwe chiphadzuŵa. Maso ako akunga ngati nkhunda. Mkazi
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taona, wakongolatu, bwenzi langa; namwaliwe taona, wakongola, maso ako akunga a nkhunda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe wokondedwa wanga, ndiwe wokongoladi! Ndithu, ndiwe chiphadzuwa, maso ako ali ngati nkhunda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taona, wakongolatu, bwenzi langa; namwaliwe taona, wakongola, Maso ako akunga a nkhunda.