Song of Solomon 1:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mitanda ya nyumba yathu ndi yamkungudza, phaso lake ndi la mtengo wa paini.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mitanda ya nyumba zathu nja mikungudza, ndi mapaso athu nga mlombwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mitanda ya nyumba yathu ndi ya mkungudza, phaso lake ndi la mtengo wa payini.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mitanda ya nyumba zathu nja mikungudza, Ndi mapaso athu nga mlombwa.