Song of Solomon 1:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mafuta ako odzola ngonunkhira bwino, dzina lako likundikumbutsa za mafuta otsanyukako. Nchifukwa chaketu, atsikana sangaleke kukukonda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mafuta ako anunkhira bwino; dzina lako likunga mafuta onunkhira otsanulidwa; chifukwa chake anamwali akukonda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mafuta ako odzola ndi onunkhira bwino; dzina lako lili ngati mafuta onunkhira otsanulidwa. Nʼchifukwa chake atsikana amakukonda!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mafuta ako anunkhira bwino; Dzina lako likunga mafuta onunkhira otsanulidwa; Cifukwa cace anamwali akukonda.