Song of Solomon 1:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tandiwuza, iwe wokondedwa wanga wapamtima, kumene umadyetsa ziŵeto zako, kumene umazigoneka masana. Nanga ndizingokhala ndili zunguliruzunguliru ku magulu a ziŵeto za abusa anzako! Mwamuna
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiuze, iwe amene moyo wanga ukukonda, umaweta kuti gulu lako? Umaligonetsa kuti pakati pa usana? Pakuti ndikhalirenji ngati wosochera pambali pa magulu a anzako?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndiwuze iwe, amene ndimakukonda, kumene umadyetsa ziweto zako ndi kumene umagoneka nkhosa zako nthawi yamasana. Ndikhalirenji ngati mkazi wachiwerewere pambali pa ziweto za abwenzi ako?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiuze, iwe amene moyo wanga ukukonda, Umaweta kuti gulu lako? Umaligonetsa kuti pakati pa usana? Pakuti ndikhalirenji ngati wosocera Pambali pa magulu a anzako?