Song of Solomon 1:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe bwenzi langa, kukongola kwako, ngati akavalo a magaleta a Farao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndakulinganiza, wokondedwa wanga mnyamatawe, ngati akavalo a magaleta a Farao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe bwenzi langa, uli ngati kavalo wamkazi ku magaleta a Farao.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndakulinganiza, wokondedwa wanga mnyamatawe, Ngati akavalo a magareta a Farao.