Song of Solomon 2:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ona, nyengo yachisanu yatha, mvula yatha ndipo yapitiratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti, taona, chisanu chatha, mvula yapita yaleka;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ona, nyengo yozizira yatha; mvula yatha ndipo yapitiratu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti, taona, cisanu catha, Mvula yapita yaleka;