Song of Solomon 2:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adanditenga kupita nane ku nyumba yaphwando, mbendera yake yozika pa ine inali chikondi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anandifikitsa kunyumba ya vinyo, mbendera yake yondizolimira inali chikondi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye wanditengera ku nyumba yaphwando, ndipo mbendera yake yozika pa ine ndi chikondi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anandifikitsa ku nyumba ya vinyo, Mbendera yace yondizolimira inali cikondi.