Song of Solomon 4:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe mlongo wanga, iwe mkazi wanga, uli ngati munda wopiringidza, ngati munda wopiringidza, ngati kasupe wochingidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mlongo wanga, mkwatibwi ndiye munda wotsekedwa; ngati kasupe wotsekedwa, ndi chitsime chopikiza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe mlongo wanga, mkwatibwi wanga, ndiwe munda wopiringidzidwa; ndiwe kasupe wotchingidwa, chitsime chotetezedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mlongwanga, mkwatibwi ndiye munda wotsekedwa; Ngati kasupe wotsekedwa, ndi citsime copikiza.