Song of Solomon 4:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumeneko mbeu zimakondwa bwino. Munda wake, ngati dimba la makangaza lokhalanso ndi zipatso zokoma zamitundumitundu, ndi maluŵa amitundumitundu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mphukira zako ndi munda wamakangaza, ndi zipatso zofunika, bonongwe ndi narido.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zomera zako ndi munda wa zipatso za makangadza; muli zipatso zokoma kwambiri, muli hena ndi nadi,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mphukira zako ndi munda wamakangaza, Ndi zipatso zofunika, bonongwe ndi mphoka,