Song of Solomon 4:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuli mitengo ndi zitsamba zosiyanasiyana zopangira zonunkhira zabwino kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Narido ndi chikasu, nzimbe ndi sinamoni, ndi mitengo yonse ya lubani; mure ndi khonje, ndi zonunkhiritsa zonse zomveka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
nadi ndi safiro, kalamusi ndi sinamoni, komanso mtengo uliwonse wonunkhira bwino. Mulinso mure ndi aloe ndi zonunkhiritsa zonse zabwino kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mphoka ndi cikasu, Nzimbe ndi ngaho, ndi mitengo yonse yamtanthanyerere; Nipa ndi khonje, ndi zonunkhiritsa zonse zomveka.